| Id |Raw text |normalised | |
| 10APR10_14|Mukupitilira kumvera nkhani mwatsatanetsatane pompano pa wayilesi ya MIJ FM Koma tisanapitilile ndi nkhanizi|Mukupitilira kumvera nkhani mwatsatanetsatane pompano pa wayilesi ya MIJ FM Koma tisanapitilile ndi nkhanizi | |
| 10APR10_15|Ndipo Mu nkhani za m’mayiko ena………… Anthu okwana makumi atatu (30) aphedwa ndi zigawenga mdziko la Nigeria.Gulu la zigawenga a mifuti, anachita chiwembu dera la Benue|Ndipo Mu nkhani za m’mayiko ena………… Anthu okwana makumi atatu (sate) aphedwa ndi zigawenga mdziko la Nigeria.Gulu la zigawenga a mifuti, anachita chiwembu dera la Benewu | |
| 10APR10_16|lachisanu sabata latha, ndipo kafukufuku wa apolisi ali akusonyeza kuti gulu lazigawengali linaombela anthu okhala mdelali|lachisanu sabata latha, ndipo kafukufuku wa apolisi ali akusonyeza kuti gulu lazigawengali linaombela anthu okhala mdelali | |
| 10APR10_17|Ngakhale gulu lomwe lachita za chiwembu-zi lisakudziwika, akuluakulu ati akukayikila anyamata oweta ziweto omwe akhala asakugwilizana ndi gulu lina la zifwamba dera-li|Ngakhale gulu lomwe lachita za chiwembu-zi lisakudziwika, akuluakulu ati akukayikila anyamata oweta ziweto omwe akhala asakugwilizana ndi gulu lina la zifwamba dera-li. | |
| 12APR10_19|Akuluakulu ena a boma ati akhala akutumiza achitetezo ochuluka m’dera-li ngati njira imodzi yothetsera kusamvanaku|Akuluakulu ena a boma ati akhala akutumiza achitetezo ochuluka m’dera-li ngati njira imodzi yothetsera kusamvanaku. | |